You are on page 1of 1

TO: .................................................

.................................................
.................................................

Date .........../2010

Okondedwa mwa Ambuye,

KUFUNA KUDZAPEPHA THANDIZO LOGULIRA UNIFORM KWA AKHRISTU ONSE


AKUFUNA KWABWINO

Ndi kulonjera mu dzina la ambuye wathu Yesu khristu.

Ife a CHIGODI CHIYANJANO CHOIR, tikupepha kwa akhristu onse akufuna kwa bwino kuti
pa ...................../2010 tikufuna tidzapephere nanu ma services onse. Chotero tikupepha ku mpingo
wonse kuti kangachepe komwe Akhristu angazakwanitse kutithandiza nako patsikuli tidzakhala
okondwa ndi othokoza.

Ndichikhulupiliro tidziwa kuti muli omasuka kutilandira patsikuli.

Ambuye akutsogolereni pamene muli kukonzeka za kubwera kwathu pa mpingo wanu patsikuli.

_______________________ _____________________ __________________


MUSIC CHAIRMAN SESSION CLARK MODERATOR

You might also like