Professional Documents
Culture Documents
Chi010 Wallchart 2012
Chi010 Wallchart 2012
Mapiritsi
Jakisoni Kondomu Lupu
a mphamvu ziwiri
• Ndi yodalirika ndiponso nkosavuta mayi kutenga • Ndi yodalilika komanso yotetezeka. • Imathandiza kupewa mimba ndi matenda ena • Kapulasitiki kakang'ono kamene kamaikidwa
mimba ngati atasiya kugwiritsa ntchito. opatsilana pogonana kuphatikizapo EDZI, m’chibelekelo cha amayi.
• Mayi amabayitsa kamodzi pa miyezi itatu iliyonse
• Imwani pilitsi limodzi tsiku lili lonse ndi kuyamba (masabata khumi ndi atatu) ndi DPMA, miyezi iwiri mukagwiritsa ntchito moyenera nthawi zonse. • Ndi yodalilika kwambiri imakhala nthawi yaitali ndipo
paketi ya tsopano panthawi yake kuti mapilitsiwo iliyonse ndi NET-EN. Mayi akhoza kuchedwerapo mayi amatenga mimba mosavuta akachotsa. Mayi atha
agwire ntchito bwino.
• Kuti atetezedwe ku matenda opatsirana pogonana kukhala nayo mpaka zaka khumi ndi ziwiri.
kudzabayitsa jakisoni ndi masabata anayi ndi DPMA
kapena masabata awiri ndi NET-EN. kuphatikiza Edzi mabanja ena amagwiritsa ntchito
• Kusamba mosayembekezera kapena modontheza makondomu pambali pa njira zina zolelera. • Lupu ikhonza kuikidwa mayi akangobereka kumene,
kukhoza kuchitika makamaka mu miyezi • Ndizothekera kukalandira jakisoni kunja kwa ngakhalenso nthawi yina ili yonse komanso akhonza
yoyambirira. Izi sizoopysa. Msambo umayamba chipatala. • Ndi yosavuta kugwilitsa ntchito ngati osatero malingana ndi njira yake ya lupu.
kuchepa komanso umachitika mu nthawi yake mwaphunzitsidwa.
pakapita miyezi ingapo. • Kusamba modukizadukiza kapena kudonthetsa • Mayi akhoza kumva kupweteka poyika Mayi akhonza
kumakhalapo miyezi ingapo yoyambirira, kenako • Ndi yodalilika mukagwilitsa ntchito moyenela kusamba kwambiri komanso kutenga nthawi yaitali
• Amayi ena amamva kupweteka kwa mutu, ena mayi amasiyirathu kusamba. Pang’ono ndi pang’ono akusamba, makamaka poyamba, Ndi njira yimeneyi mai
amaneneperako, ena amamva cham'mimba nthawi zonse. Komano anthu sakonda kuigwirisa
mayi amanenepa, amamva kupweteka mutu. Koma sataaya magazi ambiri ndipo imathandiza ku matenda
makamaka mu miyezi yoyambirira. Izi zimasiya siyodetsa nkhawa. ntchito nthawi zambiri. ochepa magazi.
pakapita kanthawi.
• Ndi yachinsinsi Anthu ena sangadziwe kuti mayi • Anthu ena amakana kondomu chifukwa • Zovuta zodetsa nkhawa sizichitikachitika Ngati mayi ali
• Ndi yabwino pafupifupi kwa mayi aliyense. Zovuta akugwilitsa ntchito njira imeneyi. imawasokoneza pogonana, imachepetsa kukoma ndi matenda opatsilana pogonana nthawi imene lupuyo
zodetsa nkhawa sizichitikachitika. kwa kugonana ndiponso imawachititsa manyazi. imaikidwa ndikwapafupi kukhala ndi matenda a
• Njirayi itha kugwiritsidwa ntchito ndi mai wa mchibelekelo.
• Ikhoza kugwiritsidwa ntchito ndi mayi wamsinkhu msinkhu wina uli onse, kaya anabelekapo kapena
wina uliwonse kaya anaberekapo kale kapena ayi. ayi. • Itha kutuluka kapena kugwa payokha makamaka
• Imathandiza kuchepetsa cham’mimba pamene mayi • Mayi akasiya kugwiritsa ntchito njirayi atha Njira Yapamkono masiku oyambilira.
akusamba, kutaya magazi ambiri posamba, kutenganso mimba, koma amayi ena • Mayi amatenga mimba mosavuta akachotsa lupu.
kuperewera kwa magazi ndi zovuta zina. amachedwelapo. Pakapita miyezi itatu, atalandira
jakisoni pakhoza kupitanso miyezi ingapo.
• Timachubu ta pulasitiki timene timaikidwa pa
• Njirayi njodalilika pamene mayi akuyamwitsa, nkono wa mayi. Palibenso china chochitika akaika
Kutseka Kwa Amayi kuyambira masabata asanu ndi imodzi mwana
atabadwa.
timachubuto pamkono.
• Njira iyi ikhonza kupangidwa mayi atangobereka • Ndi njira yodalilika pamene mayi akuyamwitsa
kumene, ngakhalenso nthawi ina ili yonse. koma akhoza kutenga mimba mosavuta akasiya
kumwa mapilitsi.
Kutseka Abambo
• Mayi amwe pilitsi limodzi tsiku lili lonse kuti Njira Yachilengedwe
atetezedwe mokwanira.
YODZIWA NTHAWI YOTENGELA MIMBA Njira yolerera ya pa pangozi
(Vasekitome) • Ngati mayi sakuyamwitsa, kudonthetsa kapena
• Awa ndi mapilitsi amene amathandiza
kusamba mosayembekezera kumachitika Izi
sizodetsa nkhawa. kupewa mimba ngati mayi angalandire
• Njirayi ndi ya muyaya Ndi ya abambo okhawo amene • Mayi amaphunzitsidwa kudziwa nthawi yomwe chithandizochi pasanapite masiku – asanu
sakufuna kudzaberekanso ana ganizani mozama angatenge mimba. chigonaniraneni ndi mwamuna
musanasankhe njirayi.
• Gwiritsani ntchito njira ina yolerera mpaka patatha
Chifunda mtima • Panthawi imeneyi banja lipewe kugonana kapena
ligwilitse ntchito kondomu.
mosadziteteza kapena kusagwiritsa ntchito
bwino njira yolerera.
miyezi itatu kuchokera tsiku limene opaleshoni ndi umuna • Ndiyodalilika mukatsatira moyenera Koma nthawi
inachitika. • Ndi njira yodalilika kwa mayi wina ali yense.
zina siyodalilika.
• Ndi njira yodalirika kwambiri pakapita miyezi itatu. • Mayi amaika chifunda mtima mkati mwa maliseche • Siimasokoneza mimba kapena kubweretsa
(koma osati kwathunthu) • Mwamuna ndi mkazi ayenera kugwirizana
ake nthawi zonse asanagonane. Akhoza kupanga pogwiritsa ntchito njirayi. zovuta kwa mwana woyembekezeredwayo
• Opaleshoni yake ndi yosavuta, yotetezeka komanso zimenezi nthawi isanakwane. ngati mayiyo ali ndi mimba kale.
yochitika mwabwino Imachitika mu mphindi zochepa • Ilibe zoopsa zina zili zonse kuthupi la munthu.
• Ndi yodalilika mukaigwiritsa ntchito bwino. • Njira zolelera ndizabwino kwambiri ngati
abambo samva kuwawa. • Njira zina zitha kukhala zovuta kugwiritsa ntchito
• Mayi ayenera kuyezedwa ziwalo za mkati kuti apeze pamene mayi wadwala malungo, kapena matenda a mwazitsatira. Chonde pezani njira yoti
• Amamva kupweteka komanso kutupa kwa masiku chifunda mtima cha saizi yabwino.
ochepa. Abambo ochepa amamvabe ululu kwa kumaliseche, atangobeleka kumene kapena mutsatire.
nthawi yayitali. • Amadwaladwala matenda a mchikozozo. akuyamwitsa.
Njira Zina Sizoyenekera Kwa Amayi Ena Malingana Ndi M’mene Umoyo Wawo Ulili
Kwa opereka njira zakulera Funsani kwa oyang; anira kuti mulandire uphungu woyenera
Kuti mudziwe zambiri za njira zolerera, alangizi za zakulera akhoza kuyan’ana mu bukhu la zakulera: A Global Handbook for Providers.
Alangizi a zakuthanzi akhoza kupeza bukhuli ndi makope ena a chosindikiza ichi kuchokera ku K4JHealth, Johns Hopkins Bloomberg School of Public
Health/Center for Communication Programs, 111 Market Place, Suite 310, Baltimore, Maryland 21202, U S A; email orders@huccp.org
Chipepalachi chalowa m’malo a chosindikiza cha kale Chosindikizachi chatheka ndi chithandizo chochokera ku Unites States Agency for International
Development, Global, GH/PRHPEC, pa mgwirizano wa Chithandizo cha nambala GPO-A- 00-08-00006-00. Chosinthidwa 2010 Johns Hopkins Bloomberg School
of Public Health Center for Communication Programs.