You are on page 1of 2

NATIONAL REGISTRATION ACT

MALAWIAN CITIZENS
CHENJEZO: Malingana ndi Gawo 43 la lamulo la kalembera wa dziko, aliyense wopeleka umboni wabodza, kapena
makalata achinyengo ndicholinga choti alembetse unzika adzaimbidwa mulandu
WARNING: In terms of Section 43 of the ACT, any person, who furnishes false information or forges any document for the

NR 1
purpose of obtaining registration shall be guilty of committing an offence.

Gawo loyamba / Part 1: Mbiri ya ofuna chiphaso cha unzika / National ID applicant details
1. Ndinu nzika ya dziko liti / Nationality NR 1
2. Ndinu nzika ya dziko lina liti / Second Nationality
11 Feb 2018

3. Tsiku lobadwa / Date of birth (DD/MM/YYYY) / / 4. Mwamuna / Male Mkazi / Female


5. Boma / District (Malo obadwira / Place of birth)
Mfumu yaikulu / TA Mudzi / Village
6. Dzina loyamba / First Name Maina ena / Other names Dzina la bambo / Surname

7. Nambala ya chiphaso choperekedwa pobadwa / Birth Certificate No. (if available)


8. Banja / Marital Status
Simunakhaleko pa banja / Never Married Muli pa Banja / Married Ukwati unatha / Divorced
Wamasiye / Widowed Munanyanyalitsana / Separated Anangochoka / Abandoned
9. Mtundu wa maso / Colour of eyes 10. Kutalika / Height (meter) 11. Lamya / Mobile phone
12. Nambala ya chiphaso choyendera (Ngati mulinacho)/ Passport No.(if available)
13. Ulumali ndi zina / Disability or any other observation
14. Dela lomwe mukukhala / Residential Address: Boma / District
Mfumu yaikulu / TA Mudzi / Village
15. Kumudzi kochokera / Permanent original home : Boma / District
Mfumu yaikulu / TA Mudzi /Village

Gawo lachiwiri / Part 2: Mbiri ya makolo / Parents details


1. Nambala ya chiphaso cha unzika cha mayi anu / Mother ID No.
2. Maina a mayi anu / Full Names of Mother
3. Mayi anu ndi nzika ya dziko liti / Mother Nationality
4. Kumudzi kwa mayi anu / Mother’s Permanent Home Address: Boma / District
Mfumu yaikulu / TA Mudzi / Village
5. Nambala ya chiphaso cha unzika cha bambo anu / Father ID No.
6. Maina a bambo anu / Full Names of Father
7. Bambo anu ndi nzika ya dziko liti / Father’s Nationality
8. Kumudzi kwa bambo anu /Father’s permanent home address: Boma / District
Mfumu yaikulu / TA Mudzi / Village

(Recommendation by witnesses / Chitsimikizo cha mboni)


Mboni yoyamba / First witness: Ine / I, ndikutsimikiza kuti zomwe
zalembedwazi ndi zoona. / hereby confirm that the information given above is correct.
First witness’ ID No./ Nambala cha chiphaso cha unzika cha mboni yoyamba
Saini / Signature: Tsiku / Date:

Mboni yachiwiri / Second witness: Ine / I, ndikutsimikiza kuti zomwe


zalembedwazi ndi zoona. / hereby confirm that the information given above is correct.
Second witness’ ID No./ Nambala cha chiphaso cha unzika cha mboni yachiwiri
Saini / Signature: Tsiku / Date:
Ine ndikutsimikizira kuti zomwe zalembedwazi ndizoona ndipo ndikuzindikira kuti ndikhoza kuimbidwa mlandu ngati ndanama / I certify
that the above information is correct and I am aware that I could face criminal prosecution if this information is incorrect in material
respect

Saini kapena chidindo cha chala chachikulu / Signature or Thumb impression

Dzina / full name: Tsiku / Date:

(Recommendation by Village Head / Chitsimikizo cha nyakwawa)


Ine, Nyakwawa / I, Village Head, ndikutsimikiza kuti zomwe zalembedwazi ndi
zoona. / hereby confirm that the information given above is correct.

Nambala cha chiphaso cha unzika cha nyakwawa / Village head’s ID No. Village head’s stamp /
Saini / Signature: Tsiku / Date: chidindo cha nyakwawa

Zikalata zotsimikiza unzika zikwanire malikisi 100 kapena kuposa apo. / Proof of citizenship. Score must be 100 or more.
Chiphaso cha unzika chopelekedwa ndi kholo lomwe Lisiti loperekedwa ndi kholo lomwe ndi nzika yomwe yalembedwa kale ndi
ndi nzika / National ID Card presented in person by makina omwewa / Receipt presented in person by biological parent, which is a
biological parent, who is a Malawian (100) Malawian and registered previously by same BRK (100)
Umboni wa nyakwawa kapena nduna yao / Personal Kalata yodindidwa yochokera kwa Nyakwawa yofokoza za kholo lanundi ana awo
testimony of Village Head and Advisor (80) / Certified and signed letter from Village Head with indication of your parent and
list of children (80)
Dzina lanu mu kaundula wa mmudzi / Name in Kalata yotsimikiza za unzika / Citizenship or Naturalized Certificate (60)
village register (80)
Kalata yodindidwa yochokera kwa Nyakwawa / Kalata ya khoti yotengera mwana (Ana omwe atengedwa ndi makolo ena omwe
Certified and signed letter from Village Head (40) ndi nzika) / A certified copy of Adoption Court Order (In the case of an adopted
child when one or both of the adopting parents are Malawian Citizens) (40)
Chiphaso chakubadwa chatsopano / New Birth Chiphaso chakubadwa chakale / Old Birth Certificate pre 2015 (30)
Certificate post 2015 (60)
Chiphaso choyendera cha ogwira ntchito ku ma ofesi Chiphaso choyendera ku maiko ena / Malawian Passport (40)
aukazembe kapena m’boma / Malawian Diplomatic /
Service Passport (70)
Chiphaso choyendetsera galimoto / Driver’s License Chiphaso chovotera / Voter Card (40)
(30)
Chiphaso chotsimikizika kuti mumalandira malipiro a Mboni zotsimikizika ziwiri zomwe ndi nzika zolembedwa kale mu kaundula ndi
pa ntchito m’boma / Government Pay Slip (30) makina omwewa (mboni zikhalepo polembetsa) / Two community witnesses
registered by same BRK (must be present when register) (100)
Chiphaso cha pa ntchito / Employment ID Card (10) Kalata ya ntchito / Employment Discharge Certificate (10)
Kalata ya ukwati / Marriage Certificate (10) Kalata yokhomera nsonkho / Tax Certificate (5)
Chiphaso kapena kalata ina iliyonse yovomerezeka / Kalata ya umboni kuchokera ku Social welfare office (Kwa ana otoledwa amene
Any other Official Document (10) ali ndi zaka 16 kapena kupitilira apo) / Letter from the Social Welfare Officer of
the District (In the case of an abandoned child who is now 16 years or above) (40)

You might also like