You are on page 1of 4

APPLICATION INSTRUCTIONS

GROUND ZERO®35
35% SUSPENSION CONCENTRATE FOR TERMITE CONTROL

ACTIVE INGREDIENTS: Imidacloprid 350g/l in a suspension concentrate for control of termites

READ LABEL COMPLETELY BEFORE USE. KEEP AWAY AND OUT OF REACH OF CHILDREN
PRECAUTIONS inside of the house in order to apply the GROUND
ZERO®35. This should only be done by professional
1. Store the bottle of GROUND ZERO®35 in a cool dark exterminators.
place, with the lid tightly always closed.
2. Read instructions completely before using this The termites target dry wood and may find their way to
product. the roof structure through cracks in the concrete and
3. Use gloves and protective clothing when using this walls. Special attention should be paid to cracks to
product. Wash your hands with soap immediately prevent further ingress of the termites. Pour or spray
after use. STANDARD DILUTION GROUND ZERO®35 solution in the
4. Make dilutions of GROUND ZERO®35 as directed. cracks before sealing them.
a. STANDARD DILUTION: 150mL GROUND
ZERO®35 / 100L of water Repeat the treatment after 6 months, after which the
b. HIGH DILUTION: 300mL GROUND ZERO®35 / treatment should be effective for up to 24 months.
100L of water
TERMITES CONTROL FOR NEW BUILDINGS
(See Figure 2:) Use the diluted solution within 24
hours after preparation. For new construction, make a HIGH DILUTION GROUND
5. Do not apply GROUND ZERO®35 solution when it is ZERO®35 solution as described above. The application
raining. Allow the soil to be relatively dry before should be done in two stages, as described below;
application to avoid unnecessary runoff of the
chemical. STAGE 1. Before the concrete slab has been laid, spray
6. Do not disturb the treated soil immediately after the hardcore layer with a HIGH DILUTION GROUND
application. ZERO®35 until wet. Do this for over the entire slab area
and immediately cover the sprayed area with damp-
DISPOSAL OF EMPTY CONTAINER proof sheeting to prevent drying or unnecessary
exposure of the GROUND ZERO®35 solution to sunlight.
When the bottle of GROUND ZERO®35 is empty, rinse it
Lay the concrete as soon as possible.
thoroughly with water 3 times, discarding the rinse water
in a disposal pit or treatment area. Do not reuse the STAGE 2. While the area around the foundation is still
empty container. The empty container may be returned exposed, pour the HIGH DILUTION GROUND ZERO®35
to the supplier for a refund of K50/ bottle. This refund solution around the foundation at the rate of 1L per
may be subject to change without notice. metre. Cover the foundation as soon as the GROUND
ZERO®35 is applied.
INSTRUCTIONS FOR USE
TREATMENT OF TERMITE MOUNDS.
GROUND ZERO®35 is for use by pest control
professionals. This product must be diluted in water at Where termites have built a mound/ chimneys, remove
the appropriate rates before application. Proper as much of the mound as possible, to expose the termite
application of GROUND ZERO®35, may be effective in holes in the ground. Using a STANDARD DILUTION
combating the termites for up to 24 months or more. GROUND ZERO®35 solution, pour up to 20L (depending
on the size of the mound) of solution into and around the
TERMITES IN EXISTING BUILDINGS.
holes of the mound. Cover the holes with soil
If the house does not have a concrete plinth around the immediately after treatment.
house, excavate a trench around the entire house,
TREATMENT OF OPEN FIELDS.
approximately 300mm (1 foot) deep and 200mm wide.
Fill the trench with river sand up to 200mm. Pour For an open field/ground, where there is termite activity,
STANDARD DILUTION GROUND ZERO®35 at the rate of 1L drill holes in the ground, of approximately 30 to 60mm in
per metre. Cover the sand by backfilling with soil (see diameter by 150mm - 300mm deep, spaced between
Figure 1:). Repeat the addition of soil as the ground 10m and 15m apart (see Figure 3:). If the ground is very
settles over the coming weeks. hard, open up the ground by ploughing it to loosen the
soil before treating the ground. Pour 1L of the STANDARD
If the house has an existing concrete plinth, drill holes
DILUTION GROUND ZERO®35 solution into each hole and
around the plinth at 300cm intervals around the entire
cover the hole with soil.
house. Pour 1 L of GROUND ZERO®35 solution in each
hole, then re-seal the holes. If there is severe infestation
of termites, use a high dilution of GROUND ZERO®35. It
may also be necessary to drill holes in the floor on the
CHICHEWA
ZOCHITA kwambiri, gwiritsani ntchito, mulingo wa GROUND ZERO
osungunulidwa mokwera. Zingakhale zofunikanso
1. Sungani botolo la GROUND ZERO®35 pamalo ozizira,
kukumba mabowo pansi, mkati mwa nyumba kuti
ndipo chivindikirocho chimatsekeredwa
mugwiritse ntchito GROUND ZERO. Izi ziyenera
nthawizonse.
kuchitidwa ndi anthu ozitsata, kapena kuti akatswiri.
2. Werengani malangizo mwathunthu musanagwiritse
ntchito mankhwalawa. Chiswe chimatsata matabwa owuma, ndipo chimatha
3. Gwiritsani ntchito magolovesi ndi zovala zoteteza kupeza njira yopita ku denga la nyumba kudzera
pogwiritsa ntchito mankhwalawa. Sambani manja mming'alu ya konkire ndi makoma. Chisamaliro
anu ndi sopo mwamsanga mutagwiritsa ntchito chapadera chiyenera kuperekedwa kwa ming'alu
mankhwalawa. kupewa, kuchulukana kwa chiswe. Thirani kapena
4. Sungunulani mankhwala a GROUND ZERO®35 kutsanulira GROUND ZERO®35 wosungunulidwa pa
motere; mlingo woyenera uja, ming'alu musanatsekemo kenako
a. MULINGO WOYENERA: 150mL GROUND musindikize.
ZERO®35 / 100L madzi
Bwerezani mankhwala pambuyo pa miyezi isanu ndi
b. MULINGO WOCHURUKIRA: 300mL
umodzi, kenako mankhwalawa akhale oyenera kwa
GROUND ZERO®35 / 100L madzi
miyezi 24.
(Onani Chithunzi 2:) Mugwiritsani ntchito
KUTETEZA CHISWE KU NYUMBA YOMANGA KUMENE
mankhwala osungunula, pasanthe maola 24.
Kumanga kwa tsopano gwiritsani ntchito mlingo wa
5. Musagwiritse ntchito mankhwala a GROUND
GROUND ZERO®35 wosungunulidwa mokwera monga
ZERO®35 pakagwa mvula. Lolani nthaka kuti ikhale
momwe tafotokozera pamwambapa. Ntchitoyi iyenera
youma musanayambe kugwiritsa ntchito popewa
kuchitika mu magawo awiri, monga momwe tafotokozera
kuthamanga kosafunikira kwa mankhwala.
m'munsimu;
6. Musasokoneze nthaka pamene mwathira
mankhwala posachedwa. GAWO 1. Musanamange konkire, thirani pamalopo
GROUND ZERO®35 osungunulidwa pa mlingo wokwera
MATAYIDWE A BOTOLO LA GROUND ZERO®35
mpakana nthakayo itanyowa kwambiri. Chitani ichi
Botolo la GROUND ZERO 350SC liribe kanthu, sukuluzani pamwamba pa dera lonselo ndipo mwamsanga
bwino ndi madzi katatu, kutaya madzi osukuluzawo mu muphimbe malowo ndi pepala la plastic, kapena kuti
dzenje kapena malo amene mukutetezawo. proof sheeting kuti muteteze GROUND ZERO®35
Musagwiritsenso ntchito botolo lopanda kanthu. Botolo wathiridwa pamalo po kudzuwa, mukatero muyike
lopandakanthu likhoza kubwezedwa kwa wogulitsa kuti konkire mwamsanga msanga.
akubwezereni K50 pa botolo lililonse. Ndondomeko iyi
GAWO 2. Pamalo amene mukufuna kupanga maziko anu
ikhoza kusinthidwa popanda kukudziwitsani.
ngati adakali poyera, thirani GROUND ZERO®35
MALANGIZO OYENELA KUCHITA wosungunuridwa pa mlingo wokwera pa ma mazikowo,
pa mlingo wa 1L pa metre ili yonse. Phimbani maziko wo
Mankhwala a GROUND ZERO®35 ndizogwiritsidwa
mukangomaliza ku thira GROUND ZERO® 35.
ntchito ndi anthu ozitsata. Mankhwalawa ofunika
kuwasungunula m'madzi pamlingo woyenera KUTETEZA CHULU CHA CHISWE.
musanayambe kugwiritsa ntchito. Kugwiritsa ntchito
Pamene chiswe chamanga chulu, phwasulani chulucho
bwino GROUND ZERO®35, kungakhale kotheka
mpakana mutapeza mabowo pa dothi lo. Pogwiritsa
polimbana ndi chiswe kwa miyezi 24 kapena kuposerapo.
ntchito mlingo woyenerera wa GROUND ZERO (thirani
CHISWE CHIMENE CHILI MNYUMBA YOTI 20L molingana ndi kukula kwa chulucho). Pamalopo
YAMANGIDWA KALE. makamaka mu mabowo. Tsekani mabowo wo ndi dothi
msanga mutathira makwalala a chiswe wo.
Ngati nyumbayi ilribe konkire kuzungulira, kumbani,
ngalande kuzungulira nyumba yonse, pafupifupi 300mm KUTETEZA CHISWE PAMALO AMENE SICHINAMANGE
(1 phazi) kuya ndi 200 mm. Thirani mngalande
Pamalo pomwe pali chiswe, pakuyenera kukumbidwa ma
yakumbidwa yo, mchenga wa ku mtsinje, mpaka
bowo pafupifupi 30 mpaka 60mm m'mbali mwake ndi
200mm. Thirani GROUND ZERO amene wasungunulidwa
150mm - 300mm chakuya, pakati pakhale, mpata wa 10
pa mlingo woyenerera, pa mlingo wa 1L pa mita iliyonse.
mpakana 15m (onani Chithunzi 3:). Ngati nthaka ili
Phimbani mchenga mwa kusamaliza nthaka (onani
yovuta, yolimba, limani pamalopo ndi plough kuti
chithunzi 1:). Bwerezerani kuwonjezera kwa nthaka
mufewetse nthaka yo musanayambe kuyithira
pamene nthaka ikukhazikika pamasabata omwe
mankhwala a GROUND ZERO. Thirani 1L ya GROUND
akubwera.
ZERO®35 yosungunula pa mlingo woyenera pa bowo
Ngati nyumba ili ndi konkire kale, kumbani mabowo pa lililonse ndipo mutseke mabowowo ndi dothi msanga .
konkiri yo ndi masentimita 300 kuzungulira nyumba
yonseyo. Thirani 1 L ya GROUND ZERO wosungunulidwa
pa mlingo woyenera mubowo lirilonse, kenaka
mutsekezenso mabowo. Ngati chiswe chawononga
DILUTION TABLE
GROUND ZERO® 35 WATER
50 ml 33 L
100 ml 67 L
150 ml 100 L
200 ml 133 L
250 ml 167 L
300 ml 200 L
350 ml 233 L
400 ml 267 L
450 ml 300 L
500 ml 333 L
550 ml 367 L
600 ml 400 L
650 ml 433 L
700 ml 467 L
750 ml 500 L
800 ml 533 L
850 ml 567 L
900 ml 600 L
950 ml 633 L
1000 ml 667 L
Figure 1: Foundation Protection
Figure 2: Dilution Table

Manufactured by:
Sulphur Mills
404/405 604/605, 349 – Business Point
Western Express Highway,
Andheri(E), Mumbai – 400069.
India

For:
Chemical Enterprise Limited
P O Box 30285
Chichiri,
Blantyre 3,
Malawi
e-mail: chemistry@chemicalsmw.com
WWW.CHEMICALSMW.COM
GROUND ZERO®35 is a registered
trademark of Chemical Enterprise
Limited

Figure 3: Field Protection

You might also like